• Wed. Jan 22nd, 2025

MWASA WARD UPDATE

Byadmin

Jul 23, 2024

Frank Raphael Maluwa

Zotsatira zosatsimikizika zikuonetaa kuti Chipani cha Malawi Congress (MCP) ndichomwe chikutsogola pachisankho chosankha Khansala ku Mwasa Ward m’boma la Mangochi.

Yemwe akuimira chipanichi Stewart Mwase akutsogola ndimavoti 1073 ndipo pambuyo pake pakubwera Adam Kida wa DPP ndimavoti 493.

Bungwe la MEC lidakawerengelabe mavoti pasukulu ya Saint Augustine 2. Bungweli lilengeza mawa zotsatira zotsimikizika ku HHI mumzinda wa Blantyre.

Author

By admin

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *